canti in chichewa

Aleluya
(lingua: Chichewa – Malawi)

A-aleluya – ah (3v) – aleluya, aleluya (2v)
Nayo nthawi yosangalala anthu
Nsembe yathu ndi Mwana wa Mulungu
Tonse lero tikhulupirire Yesu
Aleluya – aleluya

Alleluia: questo è tempo di gioia per tutti!
Diamo il benvenuto al Figlio del Signore
Crediamo in Gesù oggi e sempre! Alleluia
Alleluia: lo ringraziamo oggi e sempre,
Lo cantiamo con tutto il nostro cuore,
Ci amiamo nel nome di Gesù! Alleluia!

 

 

Nchito Za Mulungu
(lingua: Chichewa – Zambia)

Nchito za Mulungu
ndi zolenge dwa zache
Tamandani Ambuje
kulitsani iye (2v)
Maka maka
maka maka inu atumulindi nzeru
mukonda na naye
mukonda cheza naye
maka maka inu antumulindi nzeru
Tamandani Ambuye kulitsani iye
Dzuwa lowalitsa
mwezi wocezimira
Tamandani Ambuye
kulitsani iye
Ndi inu nyenyezi
pa kung’anima m’mwamba
Tamandani Ambuye kulitsani iye

Lodate Dio e rendetelo grande
in tutti i tempi e in tutti i luoghi
Soprattutto voi uomini
che siete grandi e avete intelligenza
pregate il Signore e amatevi

 

 

Amai Athu
(lingua: Chichewa – Zambia)

Amai athu Maria Woyera,
kwa Mulungu tipempherereni
atipatse mtendere mumtima
caulele, cimwemwe, Cikondi (caulele)
caulele, cimwemwe, Cikondi
Pansi pano pasanakhale munthu
wolingana ndi inu Maria
ndi kumwamba pa cimpando canu
muli nawo ulemu woposa
muli nawo ulemu woposa :
… Amai athu
Mungakhale Amai a Mulungu
munacepa pamaso pa anthu
M’ene inu mukana ulemu
ndye Mulungu akulitsa inu
ndye Mulungu akulitsa inu :
… Amai athu

Madre nostra Maria
prega per noi il Signore
che ci dia pace nel cuore
gioia e amore.
Quì sulla terra tutti gli uomini
ti rendono gloria
e nel cielo sei regina
e madre nostra Maria
Anche se sei stata madre di Dio
ti sei fatta umile davanti agli uomini
e nella tua umiltà
il Signore ti ha dato gloria.

 

 

Nchito Za Mulungu
(lingua: Chichewa – Zambia)

Nchito za Mulungu
ndi zolenge dwa zache
Tamandani Ambuje
kulitsani iye (2v)
Maka maka
maka maka inu atumulindi nzeru
mukonda na naye
mukonda cheza naye
maka maka inu antumulindi nzeru
Tamandani Ambuye kulitsani iye
Dzuwa lowalitsa
mwezi wocezimira
Tamandani Ambuye
kulitsani iye
Ndi inu nyenyezi
pa kung’anima m’mwamba
Tamandani Ambuye kulitsani iye

Lodate Dio e rendetelo grande
in tutti i tempi e in tutti i luoghi
Soprattutto voi uomini
che siete grandi e avete intelligenza
pregate il Signore e amatevi

 

 

Tate Mulungu
(lingua: Chichewa – Zambia)

Tate Mulungu
ndine Kapolo wanu
m’mene muitana ena
muitanenso ine
Musandipitilile Yesu ndine Kapolo wanu
m’mene muitana ena muitanenso ine
Tate Mulungu
ndine Kapolo wanu
m’mene muitana ena
muitanenso ine
Ine ndiri ndi njala yotumikira Mulungu
m’mene ndikalalike uthenga wanu Ambuye

Padre Dio, sono tuo servo
come chiami altri, chiama anche me
Non ignorarmi Gesù, sono tuo servo
come chiami altri, chiama anche me
Voglio servirti
nell’annunciare il tuo messaggio, Signore

 

 

Tiyeni Tinene Za Iye
(lingua: Chichewa – Zambia)

Mulungu anati kwa ife:
musabvutikeni
kuti tidzadya ciani
Ndipo tibvalenji
Tiyeni (Tiyeni) – Tinene (Tinene)
Tinene za iye (Ngakhale)
Ngakhale ena sanena
Tinene za iye
Koma moyo ndi cakudya
Upambana ndi moyo
Ndipo thupi ndi zobvala
Lipambana ndi thupi
Tisabvutike ndi zina
Za m’dziko la pansi
Atate athu adziwa
Zomwe tizisowa
Tonse tiyambe kufuna
Ufumu wa Mulungu
Ndipo zomwe tizisowa
Adzaonjezatu

Dio ci ha detto: non preoccupatevi
di cosa mangerete o di cosa vestirete
Parliamo di Lui,
anche se gli altri non parlano di Lui
Noi parliamo di Lui
Tra la vita e il cibo
ciò che è più importante è la vita
Non preoccupiamoci
delle cose di questo mondo.
Il nostro Padre conosce tutto quello
di cui abbiamo bisogno
Incominciamo tutti a cercare
il Regno di Dio,
tutto il resto ce lo darà Lui
Zikomo
(lingua: Chichewa – Malawi)
Ambuye mumatikonda
Tigwire – Tigwire tidzanja tizadaike (2v)
Ambuye (Ambuye) – zikomo (zikomo)
Tigwire – Tigwire tidzanja tisadaike (2v)
– Ambuye mumatidjetsa
Tigwire – Tigwire tidzanja tizadaike
– Ambuye ndi Mbuya wathu
Tigwire – Tigwire tidzanja tizadaike
– Ambuye ndi nyale yathu
Tigwire – Tigwire tidzanja tizadaike
– Ambuye ndi njira yathu
Tigwire – Tigwire tidzanja tizadaike

Signore Tu ci ami,
Signore (Signore) grazie (grazie)
Ti teniamo stretto a noi e non ti lasciamo
Signore Tu ci custodisci
Signore Tu ci nutri
Signore Tu sei la strada